1 Samueli 13:1 - Buku Lopatulika1 Saulo anali ndi zaka makumi atatu pamene anayamba ufumu wake; nakhala mfumu ya Israele zaka ziwiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Saulo anali ndi zaka makumi atatu pamene anayamba ufumu wake; nakhala mfumu ya Israele zaka ziwiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Saulo adaloŵa ufumu ali ndi zaka 30, ndipo adalamulira Aisraele zaka ngati 42. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Sauli analowa ufumu ali ndi zaka makumi atatu, ndipo analamulira Israeli kwa zaka 42. Onani mutuwo |