1 Samueli 12:6 - Buku Lopatulika6 Ndipo Samuele ananena ndi anthuwo, Yehova ndiye amene anaika Mose ndi Aroni, natulutsanso makolo anu m'dziko la Ejipito. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Ndipo Samuele ananena ndi anthuwo, Yehova ndiye amene anaika Mose ndi Aroni, natulutsanso makolo anu m'dziko la Ejipito. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Samuele adaŵauzanso kuti, “Chauta ndiye amene adasankha Mose ndi Aroni, kuti atulutse makolo anu m'dziko la Ejipito. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Samueli anawawuzanso kuti, “Yehova ndiye amene anasankha Mose ndi Aaroni kuti atulutse makolo anu mʼdziko la Igupto. Onani mutuwo |