1 Samueli 12:5 - Buku Lopatulika5 Ndipo iye ananena nao, Yehova ali mboni yanu, ndi wodzozedwa wake ali mboni lero kuti simunapeze kanthu m'dzanja langa. Nati iwo, Iye ali mboni. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Ndipo iye ananena nao, Yehova ali mboni yanu, ndi wodzozedwa wake ali mboni lero kuti simunapeza kanthu m'dzanja langa. Nati iwo, Iye ali mboni. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Apo Samuele adaŵauza kuti, “Chauta ndiye mboni pakati pa ine ndi inu, nayenso wodzozedwa wa Chauta ndiye mboni lero lino kuti simudandipeze chifukwa chilichonse.” Ndipo iwo adati, “Zoonadi, Chauta ndiye mboni.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Samueli anawawuza kuti, “Yehova ndiye mboni pakati pa inu ndi ine, ndiponso wodzozedwa wake ndi mboni kuti lero simunapeze chilichonse mʼdzanja langa.” Iwo anati, “Inde, Yehova ndiye mboni.” Onani mutuwo |