1 Samueli 12:7 - Buku Lopatulika7 Chifukwa chake tsono, imani pano, kuti ndiweruzane nanu pamaso pa Yehova, za ntchito zonse zolungama za Yehova anakuchitirani inu ndi makolo anu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Chifukwa chake tsono, imani pano, kuti ndiweruzane nanu pamaso pa Yehova, anakuchitirani inu ndi makolo anu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Nchifukwa chake tsono imani pomwepa, kuti tikumbutsane pamaso pa Chauta za ntchito zonse zimene Iye adachita pokupulumutsani inu ndi makolo anu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Nʼchifukwa chake tsopano imani pomwepa kuti ndikufotokozereni pamaso pa Yehova, za ntchito za chipulumutso zimene Yehova anachitira inu ndi makolo anu. Onani mutuwo |