Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




1 Samueli 12:16 - Buku Lopatulika

16 Chifukwa chake tsono, imani pano, muone chinthu ichi chachikulu Yehova adzachichita pamaso panu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

16 Chifukwa chake tsono, imani pano, muone chinthu ichi chachikulu Yehova adzachichita pamaso panu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

16 Nchifukwa chake tsono imani pomwepa, muwone chinthu chachikulu chimene Chauta akuchitireni mukupenya.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

16 “Tsono imani pomwepa kuti muone chinthu chachikulu chimene Yehova ali pafupi kuchita pamaso panu!

Onani mutuwo Koperani




1 Samueli 12:16
4 Mawu Ofanana  

Ndipo Mose ananena ndi anthu, Musaope, chilimikani, ndipo penyani chipulumutso cha Yehova, chimene adzakuchitirani lero; pakuti Aejipito mwawaona lerowa, simudzawaonanso konse.


Ndipo Israele anaiona ntchito yaikulu imene Yehova anachitira Aejipito, ndipo anthuwo anaopa Yehova; nakhulupirira Yehova ndi mtumiki wake Mose.


Chifukwa chake tsono, imani pano, kuti ndiweruzane nanu pamaso pa Yehova, za ntchito zonse zolungama za Yehova anakuchitirani inu ndi makolo anu.


Pomwepo Samuele ananena ndi Saulo, Imani, ndidzakudziwitsani chimene Yehova wanena ndi ine usiku walero. Ndipo iyeyo anati kwa iye, Nenani.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa