1 Samueli 11:13 - Buku Lopatulika13 Koma Saulo anati, Sadzaphedwa lero munthu; pakuti lero Yehova anachita chipulumutso mu Israele. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Koma Saulo anati, Sadzaphedwa lero munthu; pakuti lero Yehova anachita chipulumutso m'Israele. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Koma Saulo adati, “Palibe munthu ndi mmodzi yemwe amene aphedwe lero lino, pakuti lero Chauta wagwira ntchito yopulumutsa Aisraele.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Koma Sauli anati, “Palibe amene ati aphedwe lero, pakuti lero lino Yehova wagwira ntchito yopulumutsa Israeli.” Onani mutuwo |