1 Samueli 11:14 - Buku Lopatulika14 Ndipo Samuele ananena kwa anthuwo, Tiyeni tipite ku Giligala, kukonzanso ufumu kumeneko. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Ndipo Samuele ananena kwa anthuwo, Tiyeni tipite ku Giligala, kukonzanso ufumu kumeneko. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Tsono Samuele adauza anthuwo kuti, “Tiyeni tipite ku Giligala, tikatsimikizenso ufumu wa Saulo kumeneko.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Ndipo Samueli anati kwa anthuwo, “Tiyeni tipite ku Giligala kuti tikatsimikizenso kuti Sauli ndi mfumu yathu.” Onani mutuwo |