Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




1 Samueli 10:4 - Buku Lopatulika

4 Iwowa adzakupatsani moni, ndi kukupatsani mikate iwiri; imeneyi mudzailandira m'manja mwao.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

4 Iwowa adzakupatsani moni, ndi kukupatsani mikate iwiri; imeneyi mudzailandira m'manja mwao.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

4 Atakupatsa moni, akuninkhako mitanda iŵiri ya buledi, iwe uilandire.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

4 Adzakupatsa moni ndi kukupatsa malofu awiri a buledi. Iwe udzalandire bulediyo.

Onani mutuwo Koperani




1 Samueli 10:4
4 Mawu Ofanana  

Napatuka iwo kunkako, nafika kunyumba ya mnyamata Mleviyo, ndiyo nyumba ya Mika, namfunsa ngati ali bwanji.


Mukapitirira pamenepo tsono ndi kufika ku mtengo wathundu wa ku Tabori, kumeneko adzakomana nanu anthu atatu akukwera kwa Mulungu ku Betele, wina wonyamula anaambuzi atatu, wina mikate itatu, wina thumba la vinyo.


Ndipo m'tsogolo mwake mudzafika kuphiri la Mulungu, kumene kuli kaboma ka Afilisti; ndipo kudzali kuti pakufika inu kumzindako mudzakomana ndi gulu la aneneri, alikutsika kumsanje ndi chisakasa, ndi lingaka, ndi chitoliro, ndi zeze, pamaso pao; iwo adzanenera;


Ndipo Yese anatenga bulu namsenza mkate, ndi thumba la vinyo, ndi mwanawambuzi, nazitumiza kwa Saulo ndi Davide mwana wake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa