1 Samueli 1:25 - Buku Lopatulika25 Ndipo iwo anapha ng'ombe, nabwera naye mwanayo kwa Eli. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 Ndipo iwo anapha ng'ombe, nabwera naye mwanayo kwa Eli. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 Kumeneko adapha ng'ombe yamphongo ija ndipo mwanayo adampereka kwa Eli. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 Tsono anapha ngʼombe yamphongo ija ndi kupereka mwana uja kwa Eli. Onani mutuwo |