1 Samueli 1:24 - Buku Lopatulika24 Ndipo atamletsa kuyamwa anakwera naye, pamodzi ndi ng'ombe ya zaka zitatu, ndi efa wa ufa, ndi thumba la vinyo, nafika naye kunyumba ya Yehova ku Silo; koma mwanayo anali wamng'ono. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201424 Ndipo atamletsa kuyamwa anakwera naye, pamodzi ndi ng'ombe ya zaka zitatu, ndi efa wa ufa, ndi thumba la vinyo, nafika naye kunyumba ya Yehova ku Silo; koma mwanayo anali wamng'ono. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa24 Atamuletsa kuyamwa, adapita naye ku nyumba ya Chauta ku Silo. Adatenga ng'ombe yamphongo ya zaka zitatu, ufa wa makilogramu khumi, ndi thumba lachikopa la vinyo. Ngakhale mwanayo anali wamng'ono ndithu, adapita nayebe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero24 Atamuletsa kuyamwa, Hana anatenga mwanayo ali wachichepere, ndikupita naye ku nyumba ya Yehova ku Silo. Anatenga ngʼombe yamphongo ya zaka zitatu, ufa wa makilogalamu khumi, ndi thumba lachikopa la vinyo. Onani mutuwo |