1 Samueli 1:14 - Buku Lopatulika14 Ndipo Eli anati kwa iye, Udzaleka liti kuledzera? Chotsa vinyo wako. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Ndipo Eli anati kwa iye, Udzaleka liti kuledzera? Chotsa vinyo wako. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Tsono adamufunsa kuti, “Mai, kodi mukhala chiledzerere mpaka liti? Pitani, akayambe watha vinyo mwamwayu.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Ndipo anamufunsa Hana kuti, “Kodi mukhala chiledzerere mpaka liti? Pitani, ayambe wakuchokani vinyo mwamwayo.” Onani mutuwo |