1 Samueli 1:13 - Buku Lopatulika13 Koma Hana ananena mu mtima; milomo yake inatukula, koma mau ake sanamveke; chifukwa chake Eli anamuyesa woledzera. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Koma Hana ananena mu mtima; milomo yake inatukula, koma mau ake sanamveke; chifukwa chake Eli anamuyesa woledzera. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Hana ankalankhula chamumtima, milomo yake yokha ndiyo inkagwedezeka, koma mau ake sankamveka. Nchifukwa chake Eli adamuyesa woledzera. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Hana ankapemphera chamumtima ndipo milomo yake inkangogwedera koma mawu ake samamveka. Choncho Eli anaganiza kuti anali ataledzera. Onani mutuwo |