1 Samueli 1:12 - Buku Lopatulika12 Ndipo panali, m'mene iye analikupempherabe pamaso pa Yehova, Eli anapenyerera pakamwa pake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ndipo panali, m'mene iye analikupempherabe pamaso pa Yehova, Eli anapenyerera pakamwa pake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Iyeyo akupemphera chotero pamaso pa Chauta, Eli ankamuyang'ana pakamwa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Akupemphera choncho kwa Yehova, Eli ankamuyangʼana pakamwa. Onani mutuwo |