1 Samueli 1:10 - Buku Lopatulika10 Ndipo mkaziyo anali ndi mtima wowawa, napemphera kwa Yehova, naliratu misozi; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Ndipo mkaziyo anali ndi mtima wowawa, napemphera kwa Yehova, naliratu misozi; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Hanayo ankavutika kwambiri mumtima mwake, ndipo adapemphera kwa Chauta, akulira ndi mtima woŵaŵa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Hana anavutika mʼmoyo mwake, ndipo anapemphera kwa Yehova akulira kwambiri. Onani mutuwo |