Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




1 Mbiri 4:4 - Buku Lopatulika

4 ndi Penuwele atate wa Gedori, ndi Ezere atate wa Husa. Awa ndi ana a Huri woyamba wa Efurata atate wa Betelehemu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

4 ndi Penuwele atate wa Gedori, ndi Ezere atate wa Husa. Awa ndi ana a Huri woyamba wa Efurata atate wa Betelehemu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

4 Penuwele amene adabereka Gedori ndi Ezere amene adabereka Husa. Ameneŵa anali ana a Huri, mwana wachisamba wa Efurata ndi tate wa Betelehemu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

4 Penueli anabereka Gedori, ndipo Ezeri anabereka Husa. Awa anali ana a Huri, mwana wachisamba wa Efurata ndi abambo a Betelehemu.

Onani mutuwo Koperani




1 Mbiri 4:4
10 Mawu Ofanana  

Namwalira Azuba, ndi Kalebe anadzitengera Efurata, amene anambalira Huri.


Ana a Kalebe ndi awa: mwana wa Huri, mwana woyamba wa Efurata, Sobala atate wa Kiriyati-Yearimu.


Salima atate wa Betelehemu, Harefi atate wa Betegadere.


Ana a Salima: Betelehemu, ndi Anetofa, Ataroti-Beti-Yowabu, ndi Hazi Amanahati, ndi Azori.


Ndi mkazi wake Myuda anabala Yeredi atate wa Gedori, ndi Hebere atate wa Soko, ndi Yekutiyele atate wa Zanowa. Ndipo awa ndi ana a Bitiya mwana wamkazi wa Farao, amene Meredi anamtenga.


Iwo ndiwo a atate wa Etamu: Yezireele, ndi Isima, ndi Idibasi; ndipo dzina la mlongo wao ndiye Hazeleleponi,


Ndipo anamuka mpaka polowera ku Gedori kum'mawa kwa chigwa, kufunafuna podyetsa zoweta zao.


Ndipo Asiriya atate wa Tekowa anali nao akazi awiri: Hela, ndi Naara.


ndi Saaraimu, ndi Aditaimu, ndi Gedera, ndi Gederotaimu; mizinda khumi ndi inai pamodzi ndi midzi yao.


Pamenepo anthu onse anali kuchipata, ndi akulu, anati, Tili mboni ife. Yehova achite kuti mkazi wakulowayo m'nyumba mwako ange Rakele ndi Leya, amene anamanga nyumba ya Israele, iwo awiri; nuchite iwe moyenera mu Efurata, numveke mu Betelehemu;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa