1 Mbiri 4:5 - Buku Lopatulika5 Ndipo Asiriya atate wa Tekowa anali nao akazi awiri: Hela, ndi Naara. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Ndipo Asiriya atate wa Tekowa anali nao akazi awiri: Hela, ndi Naara. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Asuri amene adabereka Tekowa, anali ndi akazi aŵiri, Hela ndi Nara. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Asihuri abambo a Tekowa anali ndi akazi awiri, Hela ndi Naara. Onani mutuwo |