1 Mbiri 4:3 - Buku Lopatulika3 Iwo ndiwo a atate wa Etamu: Yezireele, ndi Isima, ndi Idibasi; ndipo dzina la mlongo wao ndiye Hazeleleponi, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Iwo ndiwo a atate wa Etamu: Yezireele, ndi Isima, ndi Idibasi; ndipo dzina la mlongo wao ndiye Hazeleleponi, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Ana a Huri naŵa: Etamu amene adabereka Yezireele, Isima ndi Idibasi, ndiponso mlongo wao Hazeleleponi; Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Ana a Etamu anali awa: Yezireeli, Isima ndi Idibasi. Dzina la mlongo wawo linali Hazeleliponi. Onani mutuwo |