1 Mbiri 4:2 - Buku Lopatulika2 Ndipo Reaya mwana wa Sobala anabala Yahati; ndi Yahati anabala Ahumai, ndi Lahadi. Iwo ndiwo mabanja a Azorati. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ndipo Reaya mwana wa Sobala anabala Yahati; ndi Yahati anabala Ahumai, ndi Lahadi. Iwo ndiwo mabanja a Azorati. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Reaya mwana wa Sobala adabereka Yahati, Yahati adabereka Ahumai ndi Lahadi. Ameneŵa ndiwo anali mabanja a Azorati. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Reaya mwana wa Sobala anabereka Yahati, ndipo Yahati anabereka Ahumai ndi Lahadi. Awa anali mabanja a Azorati. Onani mutuwo |