Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




1 Mbiri 4:1 - Buku Lopatulika

1 Ana a Yuda: Perezi, Hezironi, ndi Karimi, ndi Huri, ndi Sobala.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

1 Ana a Yuda: Perezi, Hezironi, ndi Karimi, ndi Huri, ndi Sobala.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

1 Ana a Yuda naŵa: Perezi, Hezironi, Karimi. Huri ndi Sobala.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

1 Ana a Yuda anali awa: Perezi, Hezironi, Karimi, Huri ndi Sobali.

Onani mutuwo Koperani




1 Mbiri 4:1
16 Mawu Ofanana  

Ndipo panali pamene iye anabweza dzanja lake, kuti, taona, mbale wake anabadwa, ndipo namwino anati, Wadziphothyolera wekha bwanji? Chifukwa chake dzina lake linatchedwa Perezi.


Ndi ana aamuna a Yuda: Eri, ndi Onani, ndi Sela, ndi Perezi, ndi Zera; koma Eri ndi Onani anafa m'dziko la Kanani. Ndi ana aamuna a Perezi ndiwo Hezironi ndi Hamuli.


Ndi Kalebe mwana wa Hezironi anabala ana ndi Azuba mkazi wake, ndi Yerioti; ndipo ana ake ndiwo Yesere, ndi Sobabu, ndi Aridoni.


Ana a Yuda ndiwo Eri, ndi Onani, ndi Sela; Batisuwa Mkanani anambalira atatu amenewa. Koma Eri mwana woyamba wa Yuda anali woipa pamaso pa Yehova, ndi Iye anamupha.


Ndi Tamara mpongozi wake anambalira Perezi ndi Zera. Ana aamuna onse a Yuda ndiwo asanu.


Ana a Perezi: Hezironi, ndi Hamuli.


Ana a Kalebe ndi awa: mwana wa Huri, mwana woyamba wa Efurata, Sobala atate wa Kiriyati-Yearimu.


Ndi ana a Karimi: Akara wovuta Israeleyo, amene analakwira choperekedwa chiperekerecho.


Ndi ana a Hezironi anambadwirawo: Yerameele, ndi Ramu, ndi Kalebe.


Ndi ana a Eliyoenai: Hodaviya, ndi Eliyasibu, ndi Pelaya, ndi Akubu, ndi Yohanani, ndi Delaya, ndi Anani, asanu ndi awiri.


Ndipo Reaya mwana wa Sobala anabala Yahati; ndi Yahati anabala Ahumai, ndi Lahadi. Iwo ndiwo mabanja a Azorati.


Ana aamuna a Yuda, ndiwo Eri ndi Onani; ndipo Eri ndi Onani anamwalira m'dziko la Kanani.


ndi Yuda anabala Perezi ndi Zera mwa Tamara; ndi Perezi anabala Hezironi; ndi Hezironi anabala Ramu;


mwana wa Aminadabu, mwana wa Admini, mwana wa Arini, mwana wa Hezironi, mwana wa Perezi, mwana wa Yuda,


Iyo ndiyo mibadwo ya Perezi; Perezi anabala Hezironi;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa