Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




1 Mafumu 7:3 - Buku Lopatulika

3 Ndipo inayalidwa ndi mkungudza pamwamba pa zipinda makumi anai mphambu zisanu zolongosoledwa pa mapanda, mzere umodzi zipinda khumi mphambu asanu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

3 Ndipo inayalidwa ndi mkungudza pamwamba pa zipinda makumi anai mphambu zisanu zolongosoledwa pa mapanda, mzere umodzi zipinda khumi mphambu asanu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

3 Pamwamba pa mitandapo panali matabwa amkungudza okuta zipinda zimene zidaamangidwa pa nsanamira 45, pa mzere uliwonse nsanamira khumi ndi zisanu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

3 Pamwamba pa mitandapo panali matabwa a mkungudza amene anaphimba zipinda zimene zinamangidwa pa nsanamira 45, pa mzere uliwonse nsanamira 15.

Onani mutuwo Koperani




1 Mafumu 7:3
3 Mawu Ofanana  

Ndipo anamanga zipinda zosanjikizana zogundana ndi khoma, kuzungulira makoma a nyumba ya Kachisi, ndi chipinda chamkati; namanga zipinda zozinga.


Anamanganso nyumba yotchedwa Nkhalango ya Lebanoni, m'litali mwake munali mikono zana limodzi, kupingasa kwake mikono makumi asanu, ndi msinkhu wake mikono makumi atatu; naisanja pa mizere inai ya mapanda amkungudza, ndi mitanda yamkungudza, ndi mitanda yamkungudza yotanthalika mapandawo.


Ndipo panali mazenera m'mizere itatuyo, zenera limodzi lopenyana ndi linzake mizere itatu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa