1 Mafumu 7:4 - Buku Lopatulika4 Ndipo panali mazenera m'mizere itatuyo, zenera limodzi lopenyana ndi linzake mizere itatu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Ndipo panali mazenera m'mizere itatuyo, zenera limodzi lopenyana ndi linzake mizere itatu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Panalinso mafuremu a mawindo mizere itatu, windo kupenyana ndi windo linzake. Mawindowo ankapenyana atatuatatu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Mazenera a nyumbayo anali mmwamba mʼmizere itatu, zenera kuyangʼanana ndi zenera linzake. Onani mutuwo |