Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




1 Akorinto 8:8 - Buku Lopatulika

8 Koma chakudya sichitivomerezetsa kwa Mulungu; kapena ngati sitidya sitisowa; kapena ngati tidya tilibe kupindulako.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 Koma chakudya sichitivomerezetsa kwa Mulungu; kapena ngati sitidya sitisowa; kapena ngati tidya tilibe kupindulako.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 Nzoona kuti chakudya sichitifikitsa pafupi ndi Mulungu. Tikapanda kudya chakudyacho, sititayapo kanthu, komanso tikachidya, sitipindulapo kanthu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 Koma chakudya sichitisendeza kufupi ndi Mulungu. Tikapanda kudya si vuto, tikadya sitisinthikanso.

Onani mutuwo Koperani




1 Akorinto 8:8
5 Mawu Ofanana  

Ndipo mmodzi anampatsa ndalama za matalente zisanu, ndi wina ziwiri, ndi wina imodzi; kwa iwo onse monga nzeru zao; namuka iye.


Pakuti ufumu wa Mulungu sukhala chakudya ndi chakumwa, koma chilungamo, ndi mtendere, ndi chimwemwe mwa Mzimu Woyera.


Zakudya ndizo za mimba, ndi mimba ndiyo ya zakudya; koma Mulungu adzathera iyi ndi izi. Koma thupi silili la chigololo, koma la Ambuye, ndi Ambuye wa thupi;


Musatengedwe ndi maphunzitso a mitundumitundu, ndi achilendo; pakuti nkokoma kuti mtima ukhazikike ndi chisomo; kosati ndi zakudya, zimene iwo adazitsata sanapindule nazo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa