1 Akorinto 8:7 - Buku Lopatulika7 Komatu chidziwitso sichili mwa onse; koma ena, ozolowera fano kufikira tsopano, adyako monga yoperekedwa nsembe kwa fano; ndipo chikumbumtima chao, popeza nchofooka, chidetsedwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Komatu chidziwitso sichili mwa onse; koma ena, ozolowera fano kufikira tsopano, adyako monga yoperekedwa nsembe kwa fano; ndipo chikumbu mtima chao, popeza nchofooka, chidetsedwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Komabe si onse amene amadziŵa zimenezi. Ena adazoloŵera kupembedza mafano, ndipo mpaka lero akamadya chakudya choperekedwa kwa mafano, amaganiza ndithu kuti chakudyacho chidaperekedwadi kwa mafano. Tsono popeza kuti ali ndi mitima yofooka, mitima yaoyo imaipitsidwa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Koma saliyense amadziwa zimenezi. Alipo ena ozolowera mafano kwambiri mwakuti akadya chakudya chotere amaganiza kuti chakudyacho chinaperekedwa nsembe kwa mafano. Ndiye poti chikumbumtima chawo nʼchofowoka chimadetsedwadi. Onani mutuwo |