Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




1 Akorinto 8:2 - Buku Lopatulika

2 Ngati wina ayesa kuti adziwa kanthu sanayambe kudziwa monga ayenera kudziwa.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

2 Ngati wina ayesa kuti adziwa kanthu sanayambe kudziwa monga ayenera kudziwa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

2 Munthu amene amadziyesa wodziŵa kanthu, ndiye kuti sakudziŵabe kwenikweni monga momwe akadayenera kudziŵira.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

2 Munthu amene amaganiza kuti amadziwa kanthu, ndiye kuti sakudziwa monga mmene amayenera kudziwira.

Onani mutuwo Koperani




1 Akorinto 8:2
9 Mawu Ofanana  

Kodi uona munthu wodziyesa wanzeru? Ngakhale chitsiru chidzachenjera koma ameneyo ai.


Pakuti sindifuna, abale, kuti mukhale osadziwa chinsinsi ichi, kuti mungadziyese anzeru mwa inu nokha, kuti kuuma mtima kunadza pang'ono pa Israele, kufikira kudzaza kwa anthu amitundu kunalowa;


Pakuti tsopano tipenya m'kalirole, ngati chimbuuzi; koma pomwepo maso ndi maso. Tsopano ndizindikira mderamdera; koma pomwepo ndidzazindikiratu, monganso ndazindikiridwa.


Munthu asadzinyenge yekha; ngati wina ayesa kuti ali wanzeru mwa inu m'nthawi ino ya pansi pano, akhale wopusa, kuti akakhale wanzeru.


Pakuti ngati wina ayesa ali kanthu pokhala ali chabe, adzinyenga yekha.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa