1 Akorinto 7:32 - Buku Lopatulika32 Koma ndifuna kuti mukhale osalabadira. Iye amene wosakwatira alabadira zinthu za Ambuye, kuti akondweretse Ambuye; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201432 Koma ndifuna kuti mukhale osalabadira. Iye amene wosakwatira alabadira zinthu za Ambuye, kuti akondweretse Ambuye; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa32 Ndidakakonda kuti pasakhale zokudetsani nkhaŵa. Munthu wosakwatira amangotekeseka ndi za Ambuye, kuganiza za m'mene angakondweretsere Ambuye. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero32 Ine ndikufuna kuti mumasuke ku nkhawa zanu. Munthu wosakwatira amangolabadira za Ambuye, mmene angakondweretsere Ambuyewo. Onani mutuwo |