1 Akorinto 7:31 - Buku Lopatulika31 ndi iwo akuchita nalo dziko lapansi, monga ngati osachititsa; pakuti maonekedwe a dziko ili apita. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201431 ndi iwo akuchita nalo dziko lapansi, monga ngati osachititsa; pakuti maonekedwe a dziko ili apita. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa31 Ndipo amene akugwiritsa ntchito zinthu zapansipano, zisaŵagwire mtima zinthuzo. Pakuti dziko lino lapansi, monga liliri tsopanomu, likupita. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero31 Amene akugwiritsa ntchito zinthu za dziko lapansi lino, akhale ngati sizikuwakhudza. Pakuti dziko lapansi lino mmene lilirimu, likupita. Onani mutuwo |