1 Akorinto 7:27 - Buku Lopatulika27 Kodi wamangika kwa mkazi? Usafune kumasuka. Kodi wamasuka kwa mkazi? Usafune mkazi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201427 Kodi wamangika kwa mkazi? Usafune kumasuka. Kodi wamasuka kwa mkazi? Usafune mkazi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa27 Kodi ndiwe wapabanja? Usayese kuthetsa banja lako. Kodi ndiwe wopanda banja? Usayese kupeza banja. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero27 Kodi ndinu wokwatira? Musalekane. Kodi ndinu wosakwatira? Musafunefune mkazi. Onani mutuwo |