1 Akorinto 7:26 - Buku Lopatulika26 Chifukwa chake ndiyesa kuti ichi ndi chokoma chifukwa cha chivuto cha nyengo ino, kuti nkwabwino kwa munthu kukhala monga ali. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 Chifukwa chake ndiyesa kuti ichi ndi chokoma chifukwa cha chivuto cha nyengo yino, kuti nkwabwino kwa munthu kukhala monga ali. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 Chifukwa cha masautso a nthaŵi ino, ndiyesa nkwabwino kuti munthu akhale monga momwe aliri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 Chifukwa cha masautso a masiku ano, ndikuganiza kuti nʼkwabwino kuti munthu akhale monga mmene alili. Onani mutuwo |