1 Akorinto 7:2 - Buku Lopatulika2 Koma chifukwa cha madama munthu yense akhale naye mkazi wa iye yekha, ndi mkazi yense akhale naye mwamuna wa iye yekha. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Koma chifukwa cha madama munthu yense akhale naye mkazi wa iye yekha, ndi mkazi yense akhale naye mwamuna wa iye yekha. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 koma kuwopa dama, mwamuna aliyense akhale ndi mkazi wakewake, ndipo mkazi aliyense akhale ndi mwamuna wakewake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Koma chifukwa choti chigololo chawanda, mwamuna aliyense akhale naye mkazi wakewake ndipo mkazi aliyense akhale naye mwamuna wakewake. Onani mutuwo |