1 Akorinto 7:3 - Buku Lopatulika3 Mwamunayo apereke kwa mkazi mangawa ake; koma modzimodzinso mkazi kwa mwamuna. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Mwamunayo apereke kwa mkazi mangawa ake; koma modzimodzinso mkazi kwa mwamuna. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Mwamuna azipereka kwa mkazi wake zomuyenerera zokhudza banja ngati mkazi wake, momwemonso mkazi azipereka kwa mwamuna wake zomuyenerera zokhudza banja ngati mwamuna wake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Mwamuna akwaniritse udindo wake wa pa banja kwa mkazi wake, ndipo chimodzimodzi mkazi kwa mwamuna wake. Onani mutuwo |