Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




1 Akorinto 4:20 - Buku Lopatulika

20 Pakuti ufumu wa Mulungu suli m'mau, koma mumphamvu. Mufuna chiyani?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

20 Pakuti ufumu wa Mulungu suli m'mau, koma mumphamvu. Mufuna chiyani?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

20 Pakuti mu Ufumu wa Mulungu chachikulu si mau chabe, koma ntchito.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

20 Pakuti ufumu wa Mulungu si mawu chabe koma mphamvu.

Onani mutuwo Koperani




1 Akorinto 4:20
8 Mawu Ofanana  

Pakuti Uthenga Wabwino sundichititsa manyazi; pakuti uli mphamvu ya Mulungu yakupulumutsa munthu aliyense wakukhulupirira; kuyambira Myuda, ndiponso Mgriki.


Pakuti ufumu wa Mulungu sukhala chakudya ndi chakumwa, koma chilungamo, ndi mtendere, ndi chimwemwe mwa Mzimu Woyera.


mu mphamvu ya zizindikiro ndi zozizwitsa, mu mphamvu ya Mzimu Woyera; kotero kuti ine kuyambira ku Yerusalemu ndi kuzungulirako kufikira ku Iliriko, ndinakwanitsa Uthenga Wabwino wa Khristu;


koma kwa iwo oitanidwa, ndiwo Ayuda ndi Agriki, Khristu mphamvu ya Mulungu, ndi nzeru ya Mulungu.


Ndipo mau anga ndi kulalikira kwanga sanakhale ndi mau okopa a nzeru, koma m'chionetso cha Mzimu ndi cha mphamvu;


Pakuti ndingakhale ndikadzitamandira kanthu kochulukira za ulamuliro (umene anatipatsa Ambuye kukumangirira, ndipo si kukugwetsera kwanu), sindidzanyazitsidwa;


kuti Uthenga Wabwino wathu sunadze kwa inu m'mau mokha, komatunso mumphamvu, ndi mwa Mzimu Woyera, ndi m'kuchuluka kwakukulu; monga mudziwa tinakhala onga otani mwa inu chifukwa cha inu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa