1 Akorinto 4:13 - Buku Lopatulika13 ponamizidwa, tipempha; takhala monga zonyansa za dziko lapansi, litsiro la zinthu zonse, kufikira tsopano. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 ponamizidwa, tipempha; takhala monga zonyansa za dziko lapansi, litsiro la zinthu zonse, kufikira tsopano. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Anthu akamatilalatira, timangoŵayankha moleza. Tasanduka onyozeka, ngati zinyatsi za dziko lapansi, ndipo mpaka tsopano anthu onse akutiyesa zinyalala. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Pamene atilalatira timayankha mwachifundo. Mpaka pano takhala ngati zinyalala za dziko, monga zakudzala za dziko lapansi. Onani mutuwo |