1 Akorinto 4:14 - Buku Lopatulika14 Sindilembera izi kukuchititsani manyazi, koma kuchenjeza inu monga ana anga okondedwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Sindilembera izi kukuchititsani manyazi, koma kuchenjeza inu monga ana anga okondedwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Ndikukulemberani zonsezi, osati kuti ndikuchititseni manyazi, koma kuti ndikulangizeni, chifukwa ndinu ana anga okondedwa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Sindikulemba izi kuti ndikuchititseni manyazi, koma kukuchenjezani monga ana anga okondedwa. Onani mutuwo |