1 Akorinto 3:8 - Buku Lopatulika8 Koma wookayo ndi wothirirayo ali amodzi; koma yense adzalandira mphotho yake ya iye yekha, monga mwa kuchititsa kwake kwa iye yekha. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Koma wookayo ndi wothirirayo ali amodzi; koma yense adzalandira mphotho yake ya iye yekha, monga mwa kuchititsa kwake kwa iye yekha. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Tsono wobzala sasiyana ndi wothirira, ndipo aliyense adzalandira mphotho yake molingana ndi ntchito imene adaigwira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Munthu wodzala ndi munthu wothirira ali ndi cholinga chimodzi, ndipo aliyense adzapatsidwa mphotho molingana ndi ntchito yake. Onani mutuwo |