1 Akorinto 2:16 - Buku Lopatulika16 Pakuti wadziwa ndani mtima wa Ambuye, kuti akamlangize Iye? Koma ife tili nao mtima wa Khristu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Pakuti wadziwa ndani mtima wa Ambuye, kuti akamlangize Iye? Koma ife tili nao mtima wa Khristu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Ndi monga Malembo anenera kuti, “Ndani adadziŵa maganizo a Ambuye, kuti athe kuŵalangiza?” Koma ife tili ndi maganizo a Khristu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Pakuti “Ndani anadziwa malingaliro a Ambuye, kuti akhoza kumulangiza Iye.” Koma tili nawo mtima wa Khristu. Onani mutuwo |