1 Akorinto 16:9 - Buku Lopatulika9 Pakuti panditsegukira pa khomo lalikulu ndi lochititsa, ndipo oletsana nafe ndi ambiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Pakuti panditsegukira pa khomo lalikulu ndi lochititsa, ndipo oletsana nafe ndi ambiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Pakuti pano mwai ulipo woti nkuchita zazikulu, ndiponsotu adani alipo ambiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 pakuti mwayi waukulu wapezeka woti nʼkugwira ntchito yaphindu, koma pali ambiri amene akutsutsana nane. Onani mutuwo |