Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




1 Akorinto 16:8 - Buku Lopatulika

8 Koma ndidzakhala ku Efeso kufikira Pentekoste.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 Koma ndidzakhala ku Efeso kufikira Pentekoste.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 Koma ndikhala ku Efeso kuno mpaka chikondwerero cha Pentekoste.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 Koma ndikhala ndili ku Efeso mpaka nthawi ya Pentekosite,

Onani mutuwo Koperani




1 Akorinto 16:8
8 Mawu Ofanana  

ndi chikondwerero cha Masika, zipatso zoyamba za ntchito zako, zimene udazibzala m'munda; ndi chikondwerero cha Kututa, pakutha chaka, pamene ututa ntchito zako za m'munda.


Ndipo iwo anafika ku Efeso, ndipo iye analekana nao pamenepo: koma iye yekha analowa m'sunagoge, natsutsana ndi Ayuda.


koma anawatsanzika, nati, Akafuna Mulungu, ndidzabwera kwa inu; ndipo anachoka ku Efeso m'ngalawa.


Ndipo panali, pamene Apolo anali ku Korinto, Paulo anapita pa maiko a pamtunda, nafika ku Efeso, napeza ophunzira ena;


Ndipo pakufika tsiku la Pentekoste, anali onse pamodzi pamalo amodzi.


Pakuti Paulo adatsimikiza mtima apitirire pa Efeso, angataye nthawi mu Asiya; pakuti anafulumira, ngati kutheka, akhale ku Yerusalemu tsiku la Pentekoste.


Ngati ndinalimbana ndi zilombo ku Efeso monga mwa munthu, ndipindulanji? Ngati akufa saukitsidwa, tidye timwe pakuti mawa timwalira.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa