1 Akorinto 16:7 - Buku Lopatulika7 Pakuti sindifuna kukuonani tsopano popitirira; pakuti ndiyembekeza kukhala ndi inu nthawi, ngati alola Ambuye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Pakuti sindifuna kukuonani tsopano popitirira; pakuti ndiyembekeza kukhala ndi inu nthawi, ngati alola Ambuye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Ulendo umenewo sindifuna kungokuwonani chidule modutsa chabe, koma ndikuyembekeza kukhala nanu kanthaŵi ndithu, Ambuye akalola. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Sindikufuna kuti ndikuoneni tsopano mongodutsa chabe, koma ndikuyembekezera kudzakhala nanu kwa kanthawi, ngati Ambuye alola. Onani mutuwo |