1 Akorinto 16:10 - Buku Lopatulika10 Koma akadza Timoteo, penyani kuti akhale ndi inu wopanda mantha; pakuti agwira ntchito ya Ambuye, monganso ine; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Koma akadza Timoteo, penyani kuti akhale ndi inu wopanda mantha; pakuti agwira ntchito ya Ambuye, monganso ine; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Ngati Timoteo afika kwanuko, samalani kuti pasakhale kanthu komdetsa nkhaŵa pakati panu, pakuti iyenso akugwira ntchito ya Ambuye, monga ine. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Ngati Timoteyo afike kwanuko, onetsetsani kuti pasakhale zina zomuchititsa mantha pamene ali pakati panu, pakuti iye akugwira ntchito ya Ambuye monga ine. Onani mutuwo |