Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




1 Akorinto 16:5 - Buku Lopatulika

5 Koma ndidzadza kwa inu, nditapyola Masedoniya; pakuti ndidzapyola Masedoniya;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 Koma ndidzadza kwa inu, nditapyola Masedoniya; pakuti ndidzapyola Masedoniya;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 Ndidzafika kwanuko nditadutsa dziko la Masedoniya, pakuti ndingodzerako ku Masedoniyako.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 Ndidzafika kwanuko nditadutsa ku Makedoniya pakuti ndikuyembekezera kudzera ku Makedoniyako.

Onani mutuwo Koperani




1 Akorinto 16:5
6 Mawu Ofanana  

Ndipo zitatha izi, Paulo anatsimikiza mu mzimu wake, atapita pa Masedoniya ndi Akaya, kunka ku Yerusalemu, kuti, Nditamuka komweko ndiyenera kuonanso ku Roma.


Pakuti kunakondweretsa a ku Masedoniya ndi Akaya kuchereza osauka a kwa oyera mtima a ku Yerusalemu.


Ndipo ngati kuyenera kwa ine kupitanso, adzapita nane.


Koma ndidzafika kwa inu msanga, akandilola Ambuye; ndipo ndidzazindikira si mau a iwo odzitukumula, koma mphamvuyi.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa