Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




1 Akorinto 15:16 - Buku Lopatulika

16 Pakuti ngati akufa saukitsidwa, Khristunso sanaukitsidwe;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

16 Pakuti ngati akufa saukitsidwa, Khristunso sanaukitsidwa;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

16 Pakuti ngati akufa sauka, Khristunso sadauke.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

16 Pakuti ngati akufa saukitsidwa, ndiye kuti nayenso Khristu sanaukitsidwe.

Onani mutuwo Koperani




1 Akorinto 15:16
5 Mawu Ofanana  

Koma ngati Mzimu wa Iye amene adaukitsa Yesu kwa akufa akhalabe mwa inu, Iye amene adaukitsa Khristu Yesu kwa akufa adzapatsanso moyo matupi anu akufa, mwa Mzimu wake wakukhala mwa inu.


Ndiponso ife tipezedwa mboni zonama za Mulungu; chifukwa tinachita umboni kunena za Mulungu kuti anaukitsa Khristu; amene sanamuukitse, ngati kuli tero kuti akufa saukitsidwa.


ndipo ngati Khristu sanaukitsidwe, chikhulupiriro chanu chili chopanda pake; muli chikhalire m'machimo anu.


Ngati si kutero, adzachita chiyani iwo amene abatizidwa chifukwa cha akufa? Ngati akufa saukitsidwa konse, abatizidwa chifukwa ninji chifukwa cha iwo?


ndi kuti anaikidwa; ndi kuti anaukitsidwa tsiku lachitatu, monga mwa malembo;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa