1 Akorinto 15:15 - Buku Lopatulika15 Ndiponso ife tipezedwa mboni zonama za Mulungu; chifukwa tinachita umboni kunena za Mulungu kuti anaukitsa Khristu; amene sanamuukitse, ngati kuli tero kuti akufa saukitsidwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Ndiponso ife tipezedwa mboni zonama za Mulungu; chifukwa tinachita umboni kunena za Mulungu kuti anaukitsa Khristu; amene sanamuukitsa, ngati kuli tero kuti akufa saukitsidwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Ngati zili choncho, ndiye kuti ndife mboni zonama, tikuchita umboni wonama m'dzina la Mulungu, ponena kuti Mulungu adaukitsa Khristu. Ngati nzoonadi kuti akufa sauka, ndiye kuti Mulungu sadamuukitse Khristuyo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Kuwonjezera pamenepa, ndiye kuti ndife mboni zabodza pa za Mulungu, pakuti tikuchita umboni kuti Mulungu anaukitsa Khristu kwa akufa. Ngati nʼzoona kuti akufa saukitsidwa, ndiye kuti Mulungu sanaukitsenso Khristu. Onani mutuwo |