Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




1 Akorinto 15:11 - Buku Lopatulika

11 Ngati ine tsono, kapena iwowa, kotero tilalikira, ndi kotero munakhulupirira.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

11 Ngati ine tsono, kapena iwowa, kotero tilalikira, ndi kotero munakhulupirira.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

11 Motero kaya ndi ineyo kaya ndi iwowo, zimene timalalika ndi zomwezo, zimene mudakhulupirira ndi zomwezonso.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

11 Tsono kaya ndi ineyo kapena iwowo, izi ndi zomwe timalalikira, ndipo izi ndi zimene munakhulupirira.

Onani mutuwo Koperani




1 Akorinto 15:11
4 Mawu Ofanana  

Koma ndi chisomo cha Mulungu ndili ine amene ndili; ndipo chisomo chake cha kwa ine sichinakhale chopanda pake, koma ndinagwirira ntchito yochuluka ya iwo onse; koma si ine, koma chisomo cha Mulungu chakukhala ndi ine.


Koma ngati Khristu alalikidwa kuti waukitsidwa kwa akufa, nanga ena mwa inu anena bwanji kuti kulibe kuuka kwa akufa?


Pakuti ndinatsimikiza mtima kuti ndisadziwe kanthu mwa inu, koma Yesu Khristu, ndi Iye wopachikidwa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa