1 Akorinto 14:9 - Buku Lopatulika9 Momwemonso inu ngati mwa lilime simupereka mau omveka bwino, kudzazindikirika bwanji chimene chilankhulidwa? Pakuti mudzakhala olankhula kumlengalenga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Momwemonso inu ngati mwa lilime simupereka mau omveka bwino, kudzazindikirika bwanji chimene chilankhulidwa? Pakuti mudzakhala olankhula kumlengalenga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Inunso chimodzimodzi: munthu angadziŵe bwanji zimene mukulankhula, ngati polankhula simunena mau omveka bwino? Pamenepo mudzangotaya mau anu pachabe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Chimodzimodzinso inu. Ngati simungayankhule mawu omveka bwino mʼchiyankhulo chanu, wina angadziwe bwanji chimene mukunena? Muzingodziyankhulira nokha. Onani mutuwo |