1 Akorinto 14:10 - Buku Lopatulika10 Ilipo, kaya, mitundu yambiri yotere ya mau padziko lapansi, ndipo palibe kanthu kasowa mau. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Ilipo, kaya, mitundu yambiri yotere ya mau pa dziko lapansi, ndipo palibe kanthu kasowa mau. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Mosapeneka konse pali zilankhulo zamitundumitundu pa dziko lapansi, ndipo palibe ndi chimodzi chomwe chimene mau ake alibe tanthauzo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Mosakayika, pali ziyankhulo zosiyanasiyana pa dziko lapansi, koma palibe nʼchimodzi chomwe chimene chilibe tanthauzo. Onani mutuwo |