Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




1 Akorinto 12:16 - Buku Lopatulika

16 Ndipo ngati khutu likati, Popeza sindili diso, sindili wa thupi; kodi silili la thupi chifukwa cha ichi?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

16 Ndipo ngati khutu likati, Popeza sindili diso, sindili wa thupi; kodi silili la thupi chifukwa cha ichi?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

16 Nanga khutu litanena kuti, “Poti sindine diso, ndiye kuti sindine chiwalo cha thupi”, kodi silikhala chiwalo cha thupi chifukwa cha chimenecho?

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

16 Ndipo ngati khutu litanena kuti, “Pakuti sindine diso, sindine chiwalo cha thupi.” Chifukwa chimenechi sichingachititse khutu kuti lisakhale chiwalo cha thupi.

Onani mutuwo Koperani




1 Akorinto 12:16
6 Mawu Ofanana  

M'chikondano cha anzanu wina ndi mnzake mukondane ndi chikondi chenicheni; mutsogolerane ndi kuchitira wina mnzake ulemu;


Pakuti ndi chisomo chapatsidwa kwa ine, ndiuza munthu aliyense wa inu, kuti asadziyese koposa kumene ayenera kudziyesa; koma aganize modziletsa yekha, monga Mulungu anagawira kwa munthu aliyense muyeso wa chikhulupiriro.


Ngati phazi likati, Popeza sindili dzanja, sindili wa thupi; kodi silili la thupi chifukwa cha ichi?


Ngati thupi lonse likadakhala diso, kukadakhala kuti kununkhiza?


Koma makamakatu ziwalozo zoyesedwa zofooka m'thupi, zifunika;


musachite kanthu monga mwa chotetana, kapena monga mwa ulemerero wopanda pake, komatu ndi kudzichepetsa mtima, yense ayese anzake omposa iye mwini;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa