Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




1 Akorinto 12:17 - Buku Lopatulika

17 Ngati thupi lonse likadakhala diso, kukadakhala kuti kununkhiza?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

17 Ngati thupi lonse likadakhala diso, kukadakhala kuti kununkhiza?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

17 Kodi thupi lonse likadakhala diso lokha, bwenzi munthu akumva bwanji? Kapena thupi lonse likadakhala khutu lokha, bwenzi munthu akununkhiza bwanji?

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

17 Kodi thupi lonse likanakhala diso, tikanamamva bwanji? Nanga thupi lonse likanakhala khutu, tikanamanunkhiza bwanji?

Onani mutuwo Koperani




1 Akorinto 12:17
8 Mawu Ofanana  

Kodi Iye wakupanga khutu ngwosamva? Kodi Iye wakuumba diso ngwosapenya?


Khutu lakumva, ndi diso lopenya, Yehova anapanga onse awiriwo.


Ndipo ngati khutu likati, Popeza sindili diso, sindili wa thupi; kodi silili la thupi chifukwa cha ichi?


Koma tsopano, Mulungu anaika ziwalo zonsezo m'thupi, monga anafuna.


Ndipo diso silingathe kunena kwa dzanja, Sindikufuna iwe, kapenanso mutu kwa mapazi, Sindikufunani inu.


Kodi ali onse atumwi? Ali aneneri onse kodi? Ali aphunzitsi onse? Ali onse ochita zozizwa?


Kale mu Israele, munthu akati afunse kwa Mulungu, ankatero kuti, Tiyeni tipite kwa mlauliyo; popeza iye wotchedwa mneneri makono ano, anatchedwa mlauli kale.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa