1 Akorinto 12:15 - Buku Lopatulika15 Ngati phazi likati, Popeza sindili dzanja, sindili wa thupi; kodi silili la thupi chifukwa cha ichi? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Ngati phazi likati, Popeza sindili dzanja, sindili wa thupi; kodi silili la thupi chifukwa cha ichi? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Nanga phazi litanena kuti, “Poti sindine dzanja, ndiye kuti sindine chiwalo cha thupi”, kodi silikhala chiwalo cha thupi chifukwa cha chimenecho? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Ngati phazi litanena kuti, “Pakuti sindine dzanja, sindine chiwalo cha thupi.” Chifukwa chimenechi sichingachititse phazi kuti lisakhale chiwalo cha thupi. Onani mutuwo |