Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




1 Akorinto 11:9 - Buku Lopatulika

9 pakutinso mwamuna sanalengedwe chifukwa cha mkazi;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

9 pakutinso mwamuna sanalengedwa chifukwa cha mkazi;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

9 Ndiponso mwamuna sadalengedwe chifukwa cha mkazi, koma mkazi ndiye adalengedwa chifukwa cha mwamuna.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

9 Ndipo mwamuna sanalengedwe chifukwa cha mkazi, koma mkazi analengedwera mwamuna.

Onani mutuwo Koperani




1 Akorinto 11:9
5 Mawu Ofanana  

Yehova Mulungu ndipo anati, Si kwabwino kuti munthu akhale yekha; ndidzampangira womthangatira iye.


Adamu ndipo anazitcha maina zinyama zonse, ndi mbalame za m'mlengalenga ndi zamoyo zonse za m'thengo: koma kwa Adamu sanapezeke womthangatira iye.


Ndipo nthitiyo anaichotsa Yehova Mulungu mwa Adamu anaipanga mkazi, ndipo ananka naye kwa Adamu.


koma mkazi chifukwa cha mwamuna; chifukwa cha ichi mkazi ayenera kukhala nao ulamuliro pamutu pake, chifukwa cha angelo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa