1 Akorinto 11:10 - Buku Lopatulika10 koma mkazi chifukwa cha mwamuna; chifukwa cha ichi mkazi ayenera kukhala nao ulamuliro pamutu pake, chifukwa cha angelo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 koma mkazi chifukwa cha mwamuna; chifukwa cha ichi mkazi ayenera kukhala nao ulamuliro pamutu pake, chifukwa cha angelo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Tsono, chifukwa cha angelo, mkazi azivala kanthu kumutu, kuti chikhale chizindikiro cha ulemu wake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Pa chifukwa ichi, ndiponso pa chifukwa cha angelo, mkazi akuyenera kukhala ndi chizindikiro cha ulamuliro wake. Onani mutuwo |